1 Mafumu 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+ Salimo 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+ Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+ Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+
34 Zimenezi zinachimwitsa nyumba yonse ya Yerobowamu,+ ndipo inayenera kuwonongedwa ndi kufafanizidwa padziko lapansi.+
5 Mwadzudzula anthu a mitundu ina,+ mwawononga oipa.+Dzina lawo mwalifafaniza mpaka kalekale, mwalifafaniza mpaka muyaya.+
28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+