2 Mafumu 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali n’kumuthira pamutu,+ ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza+ iwe kukhala mfumu+ ya Isiraeli.”’ Ukakatero, ukatsegule chitseko ndi kuthawa, usakachedwe.”
3 Ndiyeno ukatenge botolo ladothi la mafutali n’kumuthira pamutu,+ ndipo ukanene kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ndikukudzoza+ iwe kukhala mfumu+ ya Isiraeli.”’ Ukakatero, ukatsegule chitseko ndi kuthawa, usakachedwe.”