Salimo 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ng’ombe zazing’ono zamphongo zochuluka zandizungulira.+Nkhunzi zamphamvu za ku Basana zandizinga.+ Yesaya 34:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ng’ombe zamphongo zam’tchire+ zidzatsetserekera nawo kumeneko, zing’onozing’ono ndi zamphamvu zomwe.+ Dziko lawo lidzakhala magazi okhaokha, ndipo fumbi lawo lidzanona ndi mafuta.”+
12 Ng’ombe zazing’ono zamphongo zochuluka zandizungulira.+Nkhunzi zamphamvu za ku Basana zandizinga.+
7 Ng’ombe zamphongo zam’tchire+ zidzatsetserekera nawo kumeneko, zing’onozing’ono ndi zamphamvu zomwe.+ Dziko lawo lidzakhala magazi okhaokha, ndipo fumbi lawo lidzanona ndi mafuta.”+