Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungu wawatulutsa ku Iguputo.+

      Akuwayendetsa mwa liwiro la ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+

  • Deuteronomo 33:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ulemerero wake ndi wofanana ndi wa mwana wa ng’ombe wamphongo woyamba kubadwa,+

      Ndipo nyanga zake ndi nyanga za ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+

      Nyanga zimenezo adzakankha nazo anthu.+

      Adzakankha nazo anthu onse pamodzi mpaka kukafika kumalekezero a dziko lapansi.

      Nyanga zimenezo ndi anthu masauzande makumimakumi a fuko la Efuraimu,+

      Ndiponso anthu masauzande a fuko la Manase.”

  • Yobu 39:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Kodi ng’ombe yamphongo yam’tchire* imafuna kukutumikira,+

      Kapena ingagone pafupi ndi chodyeramo ziweto zako?

  • Salimo 92:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma inu mudzakweza nyanga* yanga ngati nyanga ya ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+

      Ndidzadzola mafuta abwino.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena