Numeri 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mulungu akum’tulutsa mu Iguputo.Amathamanga mwaliwiro ngati ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Adzameza anthu a mitundu ina, om’pondereza iye,+Adzakungudza mafupa awo,+ n’kudzawaswa ndi mivi yake.+
8 Mulungu akum’tulutsa mu Iguputo.Amathamanga mwaliwiro ngati ng’ombe yam’tchire yamphongo.*+Adzameza anthu a mitundu ina, om’pondereza iye,+Adzakungudza mafupa awo,+ n’kudzawaswa ndi mivi yake.+