Deuteronomo 32:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndidzaledzeretsa mivi yanga ndi magazi,+Magazi a anthu ophedwa ndi ogwidwa.Ndipo lupanga langa lidzadya nyama,+Pamodzi ndi mitu ya atsogoleri a adani.’+ Salimo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitunduyo udzaiswa ndi ndodo yachifumu yachitsulo,+Udzaiphwanya ngati mbiya yadothi, n’kukhala zidutswazidutswa.”+
42 Ndidzaledzeretsa mivi yanga ndi magazi,+Magazi a anthu ophedwa ndi ogwidwa.Ndipo lupanga langa lidzadya nyama,+Pamodzi ndi mitu ya atsogoleri a adani.’+
9 Mitunduyo udzaiswa ndi ndodo yachifumu yachitsulo,+Udzaiphwanya ngati mbiya yadothi, n’kukhala zidutswazidutswa.”+