Yeremiya 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Ukirani dziko la Merataimu. Liukireni+ ndipo muukirenso anthu a ku Pekodi.+ Apululeni ndi kuwawonongeratu. Chitani zonse zimene ndakulamulani,” watero Yehova.+
21 “Ukirani dziko la Merataimu. Liukireni+ ndipo muukirenso anthu a ku Pekodi.+ Apululeni ndi kuwawonongeratu. Chitani zonse zimene ndakulamulani,” watero Yehova.+