Yesaya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndi mauta awo, adzaphwanyaphwanya ngakhale anyamata awo.+ Iwo sadzamvera chisoni zipatso za m’mimba.+ Diso lawo silidzamvera chisoni ana aamuna. Yeremiya 50:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo a mizinda yake,+ ndipo tsiku limenelo amuna ake onse ankhondo adzaphedwa,”+ watero Yehova.
18 Ndi mauta awo, adzaphwanyaphwanya ngakhale anyamata awo.+ Iwo sadzamvera chisoni zipatso za m’mimba.+ Diso lawo silidzamvera chisoni ana aamuna.
30 Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo a mizinda yake,+ ndipo tsiku limenelo amuna ake onse ankhondo adzaphedwa,”+ watero Yehova.