Yesaya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndi mauta awo, adzaphwanyaphwanya ngakhale anyamata awo.+ Iwo sadzamvera chisoni zipatso za m’mimba.+ Diso lawo silidzamvera chisoni ana aamuna. Yeremiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+ Yeremiya 49:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo ake, ndipo amuna ake ankhondo adzawakhalitsa chete pa tsiku limenelo,”+ watero Yehova wa makamu. Yeremiya 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muwaphe ndi kusiya mitembo yawo ili paliponse m’dziko la Akasidi.+ Muwasiye mutawabaya m’misewu ya m’dzikolo.+
18 Ndi mauta awo, adzaphwanyaphwanya ngakhale anyamata awo.+ Iwo sadzamvera chisoni zipatso za m’mimba.+ Diso lawo silidzamvera chisoni ana aamuna.
21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+
26 “Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo ake, ndipo amuna ake ankhondo adzawakhalitsa chete pa tsiku limenelo,”+ watero Yehova wa makamu.
4 Muwaphe ndi kusiya mitembo yawo ili paliponse m’dziko la Akasidi.+ Muwasiye mutawabaya m’misewu ya m’dzikolo.+