Yeremiya 50:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo a mizinda yake,+ ndipo tsiku limenelo amuna ake onse ankhondo adzaphedwa,”+ watero Yehova. Yeremiya 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Muwaphe ndi kusiya mitembo yawo ili paliponse m’dziko la Akasidi.+ Muwasiye mutawabaya m’misewu ya m’dzikolo.+ Maliro 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anyamata ndi amuna okalamba+ agona pansi m’misewu.+Anamwali anga ndi anyamata anga aphedwa ndi lupanga.+Mwapha anthu pa tsiku la mkwiyo+ wanu. Onsewo mwawaphadi+ mopanda chisoni.+
30 Choncho anyamata ake adzaphedwa m’mabwalo a mizinda yake,+ ndipo tsiku limenelo amuna ake onse ankhondo adzaphedwa,”+ watero Yehova.
4 Muwaphe ndi kusiya mitembo yawo ili paliponse m’dziko la Akasidi.+ Muwasiye mutawabaya m’misewu ya m’dzikolo.+
21 Anyamata ndi amuna okalamba+ agona pansi m’misewu.+Anamwali anga ndi anyamata anga aphedwa ndi lupanga.+Mwapha anthu pa tsiku la mkwiyo+ wanu. Onsewo mwawaphadi+ mopanda chisoni.+