-
Yesaya 21:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Pakuti iwo athawa chifukwa cha malupanga, chifukwa cha lupanga losololedwa m’chimake, chifukwa cha uta wopindidwa, ndiponso chifukwa cha kukula kwa nkhondo.
-