Yeremiya 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ine ndidzatumiza anthu opeta ku Babulo kuti akamupete ndi kusiya dziko lake lili lopanda kanthu.+ Pa tsiku la tsoka lake, anthuwo adzamuukira kuchokera kumbali zonse.+ Yeremiya 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kwezerani mpanda wa Babulo mtengo wa chizindikiro.+ Wonjezerani alonda+ ndipo ikani alondawo pamalo awo. Konzekeretsani omenya nkhondo mobisalira anzawo.+ Pakuti Yehova waganiza zoti achite ndipo adzachitira anthu okhala ku Babulo zimene wanena.”+
2 Ine ndidzatumiza anthu opeta ku Babulo kuti akamupete ndi kusiya dziko lake lili lopanda kanthu.+ Pa tsiku la tsoka lake, anthuwo adzamuukira kuchokera kumbali zonse.+
12 Kwezerani mpanda wa Babulo mtengo wa chizindikiro.+ Wonjezerani alonda+ ndipo ikani alondawo pamalo awo. Konzekeretsani omenya nkhondo mobisalira anzawo.+ Pakuti Yehova waganiza zoti achite ndipo adzachitira anthu okhala ku Babulo zimene wanena.”+