Yesaya 41:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Udzapeta+ mapiri ndi zitundazo ndipo mphepo idzaziuluza.+ Mphepo yamkuntho idzaziuluzira kumalo osiyanasiyana.+ Iweyo udzasangalala chifukwa cha Yehova.+ Udzadzitama chifukwa cha Woyera wa Isiraeli.”+ Yeremiya 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+ Mateyu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”
16 Udzapeta+ mapiri ndi zitundazo ndipo mphepo idzaziuluza.+ Mphepo yamkuntho idzaziuluzira kumalo osiyanasiyana.+ Iweyo udzasangalala chifukwa cha Yehova.+ Udzadzitama chifukwa cha Woyera wa Isiraeli.”+
7 Ndipeta anthu anga ngati mbewu kuzipata za m’dzikoli. Ndithu, ndiwauluza ndi chifoloko.+ Ndiwaphera ana awo+ ndipo ndiwononga anthu anga chifukwa sanasiye kuchita zinthu zoipa.+
12 Fosholo yake youluzira mankhusu* ili m’manja mwake, ndipo malo ake opunthirapo mbewu adzawayeretseratu kuti mbee! Tirigu adzamututira m’nkhokwe,+ koma mankhusu adzawatentha+ ndi moto umene sungazimitsidwe.”