Yeremiya 51:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Mkazi wokhala mu Ziyoni adzanena kuti, ‘Chiwawa chimene achitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Yerusalemu adzanena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu okhala m’dziko la Kasidi.’”+
35 Mkazi wokhala mu Ziyoni adzanena kuti, ‘Chiwawa chimene achitira ine ndi thupi langa chigwerenso Babulo.’+ Yerusalemu adzanena kuti, ‘Magazi anga akhale pa anthu okhala m’dziko la Kasidi.’”+