Yesaya 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Babulo, amene ndi chokongoletsera maufumu,+ chinthu chokongola ndi chonyadira cha Akasidi,+ adzakhala ngati pamene Mulungu anagonjetsa Sodomu ndi Gomora.+ Yesaya 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Babulo ndidzamusandutsa malo okhala nungu* ndiponso malo a zithaphwi. Ndidzamusesa ndi tsache* la chiwonongeko,”+ watero Yehova wa makamu.
19 Babulo, amene ndi chokongoletsera maufumu,+ chinthu chokongola ndi chonyadira cha Akasidi,+ adzakhala ngati pamene Mulungu anagonjetsa Sodomu ndi Gomora.+
23 “Babulo ndidzamusandutsa malo okhala nungu* ndiponso malo a zithaphwi. Ndidzamusesa ndi tsache* la chiwonongeko,”+ watero Yehova wa makamu.