Yesaya 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Tsopano lemba zimenezi pacholembapo, iwo akuona. Uzilembe m’buku+ kuti m’tsogolo zidzakhale umboni mpaka kalekale.+ Habakuku 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Yehova anandiyankha kuti: “Lemba masomphenyawa moonekera bwino pamiyala yosema,+ kuti wowerenga mokweza awerenge mosadodoma.+ 2 Timoteyo 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+ Chivumbulutso 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mawuwo anali akuti: “Zimene uone, lemba+ mumpukutu ndi kuutumiza kumipingo 7+ yotsatirayi: wa ku Efeso,+ wa ku Simuna,+ wa ku Pegamo,+ wa ku Tiyatira,+ wa ku Sade,+ wa ku Filadefiya,+ ndi wa ku Laodikaya.”+
8 “Tsopano lemba zimenezi pacholembapo, iwo akuona. Uzilembe m’buku+ kuti m’tsogolo zidzakhale umboni mpaka kalekale.+
2 Pamenepo Yehova anandiyankha kuti: “Lemba masomphenyawa moonekera bwino pamiyala yosema,+ kuti wowerenga mokweza awerenge mosadodoma.+
16 Malemba onse anauziridwa ndi Mulungu,+ ndipo ndi opindulitsa pa kuphunzitsa,+ kudzudzula,+ kuwongola zinthu+ ndi kulangiza m’chilungamo,+
11 Mawuwo anali akuti: “Zimene uone, lemba+ mumpukutu ndi kuutumiza kumipingo 7+ yotsatirayi: wa ku Efeso,+ wa ku Simuna,+ wa ku Pegamo,+ wa ku Tiyatira,+ wa ku Sade,+ wa ku Filadefiya,+ ndi wa ku Laodikaya.”+