Yeremiya 51:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 “Ngakhale Babulo atakwera kukafika kumwamba,+ kapenanso atakweza mphamvu zake kukhala zosafikirika,+ anthu ofunkha zinthu zake ochokera kwa ine adzamupeza,”+ watero Yehova.
53 “Ngakhale Babulo atakwera kukafika kumwamba,+ kapenanso atakweza mphamvu zake kukhala zosafikirika,+ anthu ofunkha zinthu zake ochokera kwa ine adzamupeza,”+ watero Yehova.