Yeremiya 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dziko la Kasidi lidzatengedwa monga zofunkha.+ Onse ofunkha zinthu zake adzakhutira,”+ watero Yehova.
10 Dziko la Kasidi lidzatengedwa monga zofunkha.+ Onse ofunkha zinthu zake adzakhutira,”+ watero Yehova.