Yeremiya 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwanira,+ ndidzabwezera mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo zolakwa zawo.+ Ndidzabwezera zolakwa za dziko la Akasidi+ ndipo dziko lawolo lidzakhala mabwinja mpaka kalekale,’+ watero Yehova. Yeremiya 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho mitundu yonse ya anthu idzatumikira iyeyo,+ mwana wake wamwamuna ndi mdzukulu wake mpaka idzafike nthawi yoti ufumu wake uthe.+ Pamenepo, mitundu yambiri ya anthu ndi mafumu amphamvu adzamugwiritsa ntchito ngati wantchito wawo.’+
12 “‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwanira,+ ndidzabwezera mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo zolakwa zawo.+ Ndidzabwezera zolakwa za dziko la Akasidi+ ndipo dziko lawolo lidzakhala mabwinja mpaka kalekale,’+ watero Yehova.
7 Choncho mitundu yonse ya anthu idzatumikira iyeyo,+ mwana wake wamwamuna ndi mdzukulu wake mpaka idzafike nthawi yoti ufumu wake uthe.+ Pamenepo, mitundu yambiri ya anthu ndi mafumu amphamvu adzamugwiritsa ntchito ngati wantchito wawo.’+