Yeremiya 48:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “‘Tsoka iwe Mowabu!+ Anthu a Kemosi+ awonongedwa. Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi agwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.
46 “‘Tsoka iwe Mowabu!+ Anthu a Kemosi+ awonongedwa. Ana ako aamuna ndi ana ako aakazi agwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.