Numeri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tsoka iwe Mowabu! Ndithu mudzafafanizika, inu anthu a Kemosi!+Ndithudi, iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzapereka ana ake aakazi mu ukapolo kwa Sihoni, mfumu ya Aamori.
29 Tsoka iwe Mowabu! Ndithu mudzafafanizika, inu anthu a Kemosi!+Ndithudi, iye adzapangitsa ana ake aamuna kukhala othawa kwawo, ndipo adzapereka ana ake aakazi mu ukapolo kwa Sihoni, mfumu ya Aamori.