Deuteronomo 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Yehova Mulungu wanu akukulowetsani m’dziko labwino,+ dziko la zigwa* za madzi,+ akasupe ndi madzi ochuluka otuluka m’zigwa ndi m’madera a mapiri, Deuteronomo 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Limenelo ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu akulisamalira. Nthawi zonse maso+ a Yehova Mulungu wanu amakhala padziko limeneli, kuyambira kuchiyambi kwa chaka mpaka kumapeto.
7 Pakuti Yehova Mulungu wanu akukulowetsani m’dziko labwino,+ dziko la zigwa* za madzi,+ akasupe ndi madzi ochuluka otuluka m’zigwa ndi m’madera a mapiri,
12 Limenelo ndi dziko limene Yehova Mulungu wanu akulisamalira. Nthawi zonse maso+ a Yehova Mulungu wanu amakhala padziko limeneli, kuyambira kuchiyambi kwa chaka mpaka kumapeto.