Numeri 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+ Numeri 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Inu simudzalowa m’dziko limene ndinachita kukweza dzanja langa+ polumbira kuti ndidzakhala nanu mmenemo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+ Numeri 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma mwa amuna amene anakazonda dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune, adzakhalabe ndi moyo ndithu.”’”+ Numeri 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amunawo mayina awo ndi awa: Pa fuko la Yuda,+ Kalebe mwana wa Yefune, + 1 Mbiri 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ana a Kalebe+ mwana wa Yefune+ anali Iru, Ela, ndi Naamu. Mwana wa Ela anali Kenazi.
30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+
30 Inu simudzalowa m’dziko limene ndinachita kukweza dzanja langa+ polumbira kuti ndidzakhala nanu mmenemo, kupatula Kalebe mwana wa Yefune, ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
38 Koma mwa amuna amene anakazonda dzikolo, Yoswa mwana wa Nuni ndi Kalebe mwana wa Yefune, adzakhalabe ndi moyo ndithu.”’”+