Numeri 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Kalebe anayesa kukhazika anthuwo mtima pansi pamaso pa Mose ponena kuti: “Tiyeni tipite pompano, tikatenga dzikolo kukhala lathu, chifukwa tingathe kuwagonjetsa anthuwo.”+
30 Kenako Kalebe anayesa kukhazika anthuwo mtima pansi pamaso pa Mose ponena kuti: “Tiyeni tipite pompano, tikatenga dzikolo kukhala lathu, chifukwa tingathe kuwagonjetsa anthuwo.”+