-
Yoswa 14:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndinali ndi zaka 40 pamene Mose mtumiki wa Yehova anandituma kudzafufuza zokhudza dzikoli,+ kuchokera ku Kadesi-barinea. Nditabwerako ndinamuuza moona mtima zonse zimene ndinaona.+ 8 Ngakhale kuti abale anga amene ndinali nawo, anapangitsa anthu kuchita mantha kwambiri,* ine ndinatsatira Yehova Mulungu wanga ndi mtima wonse.+
-