Numeri 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Kalebe anayesa kukhazika anthuwo mtima pansi pamaso pa Mose ponena kuti: “Tiyeni tipite pompano, tikatenga dzikolo kukhala lathu, chifukwa tingathe kuwagonjetsa anthuwo.”+ Numeri 14:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yoswa+ mwana wa Nuni ndi Kalebe+ mwana wa Yefune, amene anakazonda nawo dzikolo, anangʼamba zovala zawo. 7 Iwo anauza gulu lonse la Aisiraeli kuti: “Dziko limene tinakalowamo nʼkulizonda ndi dziko labwino kwambiri.+
30 Kenako Kalebe anayesa kukhazika anthuwo mtima pansi pamaso pa Mose ponena kuti: “Tiyeni tipite pompano, tikatenga dzikolo kukhala lathu, chifukwa tingathe kuwagonjetsa anthuwo.”+
6 Ndipo Yoswa+ mwana wa Nuni ndi Kalebe+ mwana wa Yefune, amene anakazonda nawo dzikolo, anangʼamba zovala zawo. 7 Iwo anauza gulu lonse la Aisiraeli kuti: “Dziko limene tinakalowamo nʼkulizonda ndi dziko labwino kwambiri.+