Numeri 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 N’zimenenso makolo anu anachita+ ku Kadesi-barinea,+ pamene ndinawatuma kuti akazonde dziko. Deuteronomo 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Koma nonsenu munabwera kwa ine ndi kunena kuti, ‘Tiloleni titumize amuna, atsogole kukationera dzikolo ndipo adzatiuze njira imene tiyenera kudzera ndiponso mizinda imene tikapeze kumeneko.’+
22 “Koma nonsenu munabwera kwa ine ndi kunena kuti, ‘Tiloleni titumize amuna, atsogole kukationera dzikolo ndipo adzatiuze njira imene tiyenera kudzera ndiponso mizinda imene tikapeze kumeneko.’+