Numeri 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+ Numeri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+
30 Pamenepo Kalebe+ anayesa kukhalitsa chete anthuwo pamaso pa Mose, kenako anati: “Tiyeni tipite tsopano lino, tikalanda dzikolo, pakuti tikaligonjetsa ndithu.”+
6 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni,+ ndi Kalebe mwana wa Yefune,+ amene anakazonda nawo dzikolo, anang’amba zovala zawo.+