Ekisodo 23:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Sindidzawathamangitsa pamaso pako m’chaka chimodzi, kuti dzikolo lingakhale bwinja ndi kuti zilombo zakutchire zingachuluke ndi kukuvutitsa.+ Ekisodo 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndidzawathamangitsa pamaso pako pang’onopang’ono kufikira mutaberekana ndi kulanda dzikolo.+ Salimo 105:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pang’onopang’ono anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Ndipo zipatso za ntchito imene mitundu ya anthu inagwira mwakhama, anazitenga kukhala zawo,+
29 Sindidzawathamangitsa pamaso pako m’chaka chimodzi, kuti dzikolo lingakhale bwinja ndi kuti zilombo zakutchire zingachuluke ndi kukuvutitsa.+
44 Pang’onopang’ono anawapatsa mayiko a anthu a mitundu ina,+Ndipo zipatso za ntchito imene mitundu ya anthu inagwira mwakhama, anazitenga kukhala zawo,+