1 Samueli 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chonde, usadzasiye kusonyeza nyumba yanga kukoma mtima kosatha mpaka kalekale.+ Ngakhalenso pamene Yehova adzawononga mdani aliyense wa Davide padziko lapansi,
15 Chonde, usadzasiye kusonyeza nyumba yanga kukoma mtima kosatha mpaka kalekale.+ Ngakhalenso pamene Yehova adzawononga mdani aliyense wa Davide padziko lapansi,