2 Samueli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense wotsala wa m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani.”+ 2 Samueli 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma mfumu inamvera chisoni Mefiboseti+ mwana wamwamuna wa Yonatani, mwana wa Sauli, chifukwa cha lumbiro+ limene Davideyo ndi Yonatani mwana wa Sauli anachita pakati pawo pamaso pa Yehova.
9 Ndiyeno Davide ananena kuti: “Kodi pali aliyense wotsala wa m’nyumba ya Sauli? Ndikufuna kumusonyeza kukoma mtima kosatha+ chifukwa cha Yonatani.”+
7 Koma mfumu inamvera chisoni Mefiboseti+ mwana wamwamuna wa Yonatani, mwana wa Sauli, chifukwa cha lumbiro+ limene Davideyo ndi Yonatani mwana wa Sauli anachita pakati pawo pamaso pa Yehova.