Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 19:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kenako Yehova anamuuza kuti: “Nyamuka, bwerera udzere kuchipululu cha Damasiko.+ Pita ukadzoze+ Hazaeli+ kuti akhale mfumu ya Siriya.

  • 2 Mafumu 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Hazaeli atamva mawu amenewa, anati: “Ndine ndani ine mtumiki wanu, galu ngati ine,+ kuti ndichite zinthu zazikulu ngati zimenezi?” Koma Elisa anati: “Yehova wandionetsa iweyo utakhala mfumu ya Siriya.”+

  • 2 Mafumu 10:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.

  • Amosi 1:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndidzatumiza moto+ panyumba ya Hazaeli,+ ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Beni-hadadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena