1 Mbiri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa, ndipo anawalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.
18 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa, ndipo anawalanda mzinda wa Gati+ ndi midzi yake yozungulira.