Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+ 2 Timoteyo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Uziwakumbutsa+ zimenezi nthawi zonse. Uziwachenjeza mwamphamvu+ pamaso pa Mulungu,+ kuti asamakangane pa mawu.+ Kuchita zimenezo kulibe phindu m’pang’ono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera. Tito 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zopanda pake,+ ndi opotoza maganizo a ena, makamaka amene akusungabe mdulidwe+ pakati pa anthu amenewa. Tito 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma iwe pewa mafunso opusa,+ kukumba mibadwo ya makolo,+ mikangano+ ndi kulimbana pa za Chilamulo,+ chifukwa zimenezi n’zosapindulitsa ndiponso n’zachabechabe. Tito 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 podziwa kuti munthu wotero wapotozedwa ndipo amadziimba mlandu chifukwa akudziwa kuti akuchimwa.+
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
14 Uziwakumbutsa+ zimenezi nthawi zonse. Uziwachenjeza mwamphamvu+ pamaso pa Mulungu,+ kuti asamakangane pa mawu.+ Kuchita zimenezo kulibe phindu m’pang’ono pomwe chifukwa kumawononga chikhulupiriro cha omvetsera.
10 Pakuti pali anthu ambiri osalamulirika, olankhula zopanda pake,+ ndi opotoza maganizo a ena, makamaka amene akusungabe mdulidwe+ pakati pa anthu amenewa.
9 Koma iwe pewa mafunso opusa,+ kukumba mibadwo ya makolo,+ mikangano+ ndi kulimbana pa za Chilamulo,+ chifukwa zimenezi n’zosapindulitsa ndiponso n’zachabechabe.