Miyambo 28:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Munthu wonyada amayambitsa mikangano,+ koma wodalira Yehova adzanenepa.+ Agalatiya 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngati wina akudziona kuti ndi wofunika pamene si wotero,+ akudzinyenga. 1 Timoteyo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+
6 Asakhale wotembenuka kumene,+ kuopera kuti angakhale wotukumuka chifukwa cha kunyada,+ n’kulandira chiweruzo chofanana ndi chimene Mdyerekezi analandira.+