Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti mwa kukoma mtima kwakukulu kumene ndinapatsidwa, ndikuuza aliyense wa inu kumeneko kuti musamadziganizire kuposa mmene muyenera kudziganizira.+ Koma aliyense aziganiza m’njira yakuti akhale munthu woganiza bwino,+ malinga ndi chikhulupiriro+ chimene Mulungu wamupatsa.+

  • 1 Akorinto 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ngati wina akuganiza kuti akudziwa za chinachake,+ sanachidziwebe mokwanira.+

  • 2 Akorinto 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Sitinganene kuti ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha mphamvu zathu,+ koma ndife oyenera kugwira ntchito imeneyi chifukwa cha Mulungu,+

  • 2 Akorinto 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndakhala wodzikweza tsopano. Ndinu mwandikakamiza+ kukhala wotero, popeza simunanene za zinthu zabwino zimene ndachita, ngakhale kuti munayenera kutero. Pakuti sindinachepe mwanjira ina iliyonse kwa atumwi anu apamwambawo,+ ngakhale kuti si ine kanthu m’maso mwanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena