1 Samueli 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Apanso Sauli anachita mantha kwambiri ndi Davide, moti anali kudana ndi Davide nthawi zonse.+ 1 Samueli 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukaonetsetse ndi kutsimikizira za malo onse obisika kumene iye amabisala. Kenako mudzabwerenso kwa ine ndi umboni, ndipo ine ndidzapita nanu. Ngati alidi m’dzikolo, ndidzam’funafuna mosamala pakati pa anthu masauzande+ ambirimbiriwo a Yuda.”
23 Mukaonetsetse ndi kutsimikizira za malo onse obisika kumene iye amabisala. Kenako mudzabwerenso kwa ine ndi umboni, ndipo ine ndidzapita nanu. Ngati alidi m’dzikolo, ndidzam’funafuna mosamala pakati pa anthu masauzande+ ambirimbiriwo a Yuda.”