Yoswa 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wansembe Pinihasi,+ atsogoleri a khamu la Aisiraeli+ kapena kuti atsogoleri a masauzande a Aisiraeli amene anali naye, atamva mawu amene ana a Rubeni, ana a Gadi ndi ana a Manase ananena, anakhutira nawo mawuwo. 1 Samueli 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma inu, lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani m’masautso anu onse ndi m’zowawa zanu, kufika ponena kuti: “Ife tikufuna kuti utiikire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova malinga ndi mafuko anu+ ndi mabanja anu.’”*
30 Wansembe Pinihasi,+ atsogoleri a khamu la Aisiraeli+ kapena kuti atsogoleri a masauzande a Aisiraeli amene anali naye, atamva mawu amene ana a Rubeni, ana a Gadi ndi ana a Manase ananena, anakhutira nawo mawuwo.
19 Koma inu, lero mwakana Mulungu wanu+ amene anakupulumutsani m’masautso anu onse ndi m’zowawa zanu, kufika ponena kuti: “Ife tikufuna kuti utiikire mfumu yoti izitilamulira.” Tsopano imani pamaso pa Yehova malinga ndi mafuko anu+ ndi mabanja anu.’”*