1 Samueli 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno masiku amenewo zinachitika kuti Afilisiti anayamba kusonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Isiraeli.+ Choncho, Akisi anauza Davide kuti: “Ndikukhulupirira kuti ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita ndi ine kunkhondo.”+ 1 Samueli 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Olamulira ogwirizana+ a Afilisiti anali kudutsa m’magulu a asilikali 100, ndi 1,000, ndipo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anadutsa pambuyo pawo limodzi ndi Akisi.+
28 Ndiyeno masiku amenewo zinachitika kuti Afilisiti anayamba kusonkhanitsa asilikali awo kuti akamenyane ndi Isiraeli.+ Choncho, Akisi anauza Davide kuti: “Ndikukhulupirira kuti ukudziwa kuti iwe ndi anthu ako muyenera kupita ndi ine kunkhondo.”+
2 Olamulira ogwirizana+ a Afilisiti anali kudutsa m’magulu a asilikali 100, ndi 1,000, ndipo Davide ndi amuna amene anali kuyenda naye anadutsa pambuyo pawo limodzi ndi Akisi.+