1 Samueli 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo Davide anauza Akisi kuti: “Ndiponso inu mukudziwa bwino zimene mtumiki wanu ayenera kuchita.” Chotero Akisi anauza Davide kuti: “Ndidzakuika kukhala msilikali wondilondera nthawi zonse.”+
2 Pamenepo Davide anauza Akisi kuti: “Ndiponso inu mukudziwa bwino zimene mtumiki wanu ayenera kuchita.” Chotero Akisi anauza Davide kuti: “Ndidzakuika kukhala msilikali wondilondera nthawi zonse.”+