2 Samueli 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho akulu onse+ a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni, ndipo Mfumu Davide anachita nawo pangano+ ku Heburoni pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza+ Davide kukhala mfumu ya Isiraeli.+ 1 Mbiri 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Afilisiti anamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli yense.+ Choncho Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide.+ Davide atamva zimenezi, anapita kukamenyana nawo. Salimo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+
3 Choncho akulu onse+ a Isiraeli anabwera kwa mfumu ku Heburoni, ndipo Mfumu Davide anachita nawo pangano+ ku Heburoni pamaso pa Yehova. Kenako iwo anadzoza+ Davide kukhala mfumu ya Isiraeli.+
8 Tsopano Afilisiti anamva kuti Davide amudzoza kukhala mfumu ya Isiraeli yense.+ Choncho Afilisiti onse anabwera kudzafunafuna Davide.+ Davide atamva zimenezi, anapita kukamenyana nawo.
2 Mafumu a dziko lapansi aima pamalo awo,+Ndipo nduna zapamwamba zasonkhana pamodzi mogwirizana.+Atero kuti alimbane ndi Yehova+ komanso wodzozedwa wake.+