Machitidwe 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atamuchotsa ameneyu,+ anawapatsa Davide monga mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ine ndikufuna.’+
22 Atamuchotsa ameneyu,+ anawapatsa Davide monga mfumu yawo.+ Iyeyu Mulungu anamuchitira umboni kuti, ‘Ndapeza Davide mwana wa Jese,+ munthu wapamtima panga.+ Ameneyu adzachita zonse zimene ine ndikufuna.’+