1 Samueli 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Davide analanditsa zonse zimene Aamaleki anatenga,+ n’kulanditsanso akazi ake awiri aja.