Genesis 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno Yehova anavumbitsa sulufule ndi moto kuchokera kwa Yehova kumwamba, kuvumbira pa Sodomu ndi Gomora.+ Ezekieli 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndidzapereka chiweruzo m’dziko la Mowabu,+ ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+ Amosi 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Mowabu+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.+
24 Ndiyeno Yehova anavumbitsa sulufule ndi moto kuchokera kwa Yehova kumwamba, kuvumbira pa Sodomu ndi Gomora.+
2 “Yehova wanena kuti, ‘“Popeza kuti Mowabu+ anapanduka mobwerezabwereza, sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anatentha mafupa a mfumu ya Edomu kuti apeze laimu.+