Ekisodo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo pamene amuna anali kuimba, Miriamu anathirira mang’ombe kuti:+ “Imbirani Yehova+ pakuti wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.”+ Oweruza 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa tsiku limenelo, Debora+ ndi Baraki+ mwana wa Abinowamu,+ anayamba kuimba nyimbo,+ ndipo anati:
21 Ndipo pamene amuna anali kuimba, Miriamu anathirira mang’ombe kuti:+ “Imbirani Yehova+ pakuti wakwezeka koposa.+Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.”+