Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 16:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndithudi ndikukuuzani, Mudzagwetsa misozi ndi kulira mofuula, koma dzikoli lidzasangalala. Mudzamva chisoni,+ koma chisoni chanu adzachisandutsa chimwemwe.+

  • Aroma 12:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Sangalalani ndi anthu amene akusangalala.+ Lirani ndi anthu amene akulira.

  • 2 Akorinto 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndipo taonani zimene chisoni chogwirizana ndi chifuniro cha Mulungu+ chimenechi chakuchitirani. Chakuchititsani kukhala akhama kwambiri, chakuchititsani kudziyeretsa, kuipidwa, mantha, kufunitsitsa kulapa, kudzipereka, ndiponso kukonza cholakwacho.+ Mwanjira ina iliyonse, munasonyeza kuti ndinu oyera pa nkhani imeneyi.

  • Yakobo 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Imvani chisoni ndipo lirani.+ Kuseka kwanu kusanduke kulira, ndipo chisangalalo chanu chisanduke chisoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena