Luka 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Tsoka inu amene mukukhuta tsopano, chifukwa mudzamva njala.+ “Tsoka inu amene mukuseka tsopano, chifukwa mudzamva chisoni ndi kulira.+ Chivumbulutso 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwe ukunena kuti: “Ndine wolemera,+ ndapeza chuma chambiri ndipo sindikusowa kanthu,” koma sukudziwa kuti ndiwe wovutika, womvetsa chisoni, wosauka, wakhungu,+ ndi wamaliseche.
25 “Tsoka inu amene mukukhuta tsopano, chifukwa mudzamva njala.+ “Tsoka inu amene mukuseka tsopano, chifukwa mudzamva chisoni ndi kulira.+
17 Iwe ukunena kuti: “Ndine wolemera,+ ndapeza chuma chambiri ndipo sindikusowa kanthu,” koma sukudziwa kuti ndiwe wovutika, womvetsa chisoni, wosauka, wakhungu,+ ndi wamaliseche.