Yeremiya 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tagona pansi mwamanyazi+ ndipo manyazi athuwo akupitiriza kutiphimba.+ Zimenezi zakhala choncho chifukwa chakuti ifeyo ndi makolo athu, tachimwira Yehova Mulungu wathu+ ndipo sitinamvere mawu a Yehova Mulungu wathu+ kuyambira tili anyamata mpaka lero.”+ Yeremiya 50:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “M’masiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo+ ana a Isiraeli pamodzi ndi ana a Yuda adzabwera,”+ watero Yehova. “Iwo adzayenda akulira+ ndipo adzafunafuna Yehova Mulungu wawo.+ Machitidwe 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Tsopano iwo atamva mawu amenewa, anavutika kwambiri mumtima,+ ndipo anafunsa Petulo ndi atumwi enawo kuti: “Amuna inu, abale athu, tichite chiyani pamenepa?”+
25 Tagona pansi mwamanyazi+ ndipo manyazi athuwo akupitiriza kutiphimba.+ Zimenezi zakhala choncho chifukwa chakuti ifeyo ndi makolo athu, tachimwira Yehova Mulungu wathu+ ndipo sitinamvere mawu a Yehova Mulungu wathu+ kuyambira tili anyamata mpaka lero.”+
4 “M’masiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo+ ana a Isiraeli pamodzi ndi ana a Yuda adzabwera,”+ watero Yehova. “Iwo adzayenda akulira+ ndipo adzafunafuna Yehova Mulungu wawo.+
37 Tsopano iwo atamva mawu amenewa, anavutika kwambiri mumtima,+ ndipo anafunsa Petulo ndi atumwi enawo kuti: “Amuna inu, abale athu, tichite chiyani pamenepa?”+