Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndipo inu musachite pangano ndi anthu okhala m’dziko ili,+ m’malomwake mugwetse maguwa awo ansembe.’+ Koma inu simunamvere mawu anga.+ N’chifukwa chiyani mwachita zimenezi?+

  • Yesaya 48:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Komanso, inu simunafune kumva+ kapena kumvetsa zimenezi. Kuyambira pa nthawi imeneyo kupita m’tsogolo, simunatsegule khutu lanu. Pakuti ine ndinkadziwa ndithu kuti inu munali kuchita zachinyengo,+ ndipo mwatchedwa ‘wochimwa chibadwire.’+

  • Yeremiya 22:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndinalankhula nawe pamene unali pa ufulu,+ koma iwe unandiyankha kuti, ‘Sindidzamvera.’+ Wakhala ukuchita zimenezi kuyambira uli wachinyamata, moti sunamvere mawu anga.+

  • Danieli 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Sitinamvere mawu anu, inu Yehova Mulungu wathu, mwa kuyenda motsatira malamulo anu amene munatiikira kudzera mwa atumiki anu, aneneri.+

  • 1 Akorinto 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tisamachite dama,+ mmene ena mwa iwo anachitira dama, n’kufa 23,000 tsiku limodzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena