Yesaya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ayi, inu simunamve+ kapena kudziwa zimenezi,Ndipo mʼmbuyomu makutu anu anali osatseguka, Chifukwa ndikudziwa kuti inu ndi achinyengo,+Ndipo kuyambira pamene munabadwa mumatchedwa wochimwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 48:8 Yesaya 2, ptsa. 125-126
8 Ayi, inu simunamve+ kapena kudziwa zimenezi,Ndipo mʼmbuyomu makutu anu anali osatseguka, Chifukwa ndikudziwa kuti inu ndi achinyengo,+Ndipo kuyambira pamene munabadwa mumatchedwa wochimwa.+